Home

Deralanga  ndi dongosolo limene lapangidwa kuti lipereke njira yotetezeka, yosavuta kufikika, komanso yosungira chinsinsi kwa mamembala a m’dera kuti alengeze madandaulo, ziphuphu, kapena mavuto a ntchito zomwe zikuperekedwa mwachindunji ku khonsolo ya dera.

Za Chitukuko

Za ukhondo

PEREKANI MAGANIZO

Please enable JavaScript in your browser to complete this form.
Dzina
Click or drag a file to this area to upload.
ikani umboni apa

Ubwino wogwiritsa njira imeneyi

Njira imeneyi imathandiza nzika kufotokozera nkhawa zawo mwachindunji ku ma council a m’madera. Malipoti onse amaoneka kwa akuluakulu oyenerera ndipo amatengedwa mozama.